1 Mafumu 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Geberi mwana wa Uri ku dziko la Gileadi, dziko la Sihoni mfumu ya Aamori, ndi la Ogi mfumu ya Basani; munalibe kapitao wina m'deramo.

1 Mafumu 4

1 Mafumu 4:10-23