1 Mafumu 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, Yehova Inu Mulungu wanga, mwalonga ine kapolo wanu ufumu m'malo mwa atate wanga Davide, koma ine ndine kamwana, sindidziwa kuturuka kapena kulowa.

1 Mafumu 3

1 Mafumu 3:1-15