1 Mafumu 3:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mfumu inati, Uyu akuti, Wamoyoyu ndiye mwana wanga ndi wakufayu ndiye mwana wako; ndipo winayo akuti, lai, koma mwana wako ndiye wakufayu, ndi mwana wanga ndiye wamoyoyu.

1 Mafumu 3

1 Mafumu 3:14-28