1 Mafumu 3:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anauka pakati pa usiku, natenga mwana wanga kumimba kwanga, mdzakazi wanu ndiri m'tulo, namuika m'mfukato mwace, naika mwana wace wakufa m'mfukato mwanga.

1 Mafumu 3

1 Mafumu 3:11-25