1 Mafumu 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ukadzayenda m'njira zanga kusunga malemba anga ndi malamulo anga, monga atate wako Davide anayendamo, Ine ndidzacurukitsa masiku ako.

1 Mafumu 3

1 Mafumu 3:12-24