1 Mafumu 22:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ahaziya mwana wa Ahabu anayamba kukhala mfumu ya Israyeli pa Samaria m'caka cakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri ca Yehosafati mfumu ya Yuda; nakhala mfumu ya Israyeli zaka ziwiri.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:49-53