1 Mafumu 22:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Ahaziyamwana wa Ahabu ananena ndi Yehosafati, Anyamata anga amuke pamodzi ndi anyamata anu m'zombo. Koma Yehosafati anakana.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:44-51