1 Mafumu 22:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Israyeli ananena ndi anyamata ace, nati, Kodi simudziwa kuti Ramoti Gileadi ngwathu, ndipo tangokhala cete, osaulanditsa m'dzanja la mfumu ya Aramu.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:1-6