1 Mafumu 22:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Zedekiya mwana wa Kenana anasendera, napanda Mikaya patsaya, nati, Mzimu wa Yehova wandicokera bwanji, kulankhula ndi iwe?

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:17-29