1 Mafumu 22:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Ndinaona Aisrayeli onse obalalika pamapiri ngati nkhosa zopanda mbusa; ndipo Yehova anati, Izi ziribe mwini, yense abwerere ndi mtendere ku nyumba yace.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:12-24