1 Mafumu 22:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atafika kwa mfumu, mfumu inati kwa iye, Mikaya, kodi tizimuka ku Ramoti Gileadi kukathira nkhondo, kapena tileke? Nati iye, Kwerani, ndipo mudzacita mwai, popeza Yehova adzaupereka m'dzanja la mfumu.

1 Mafumu 22

1 Mafumu 22:11-19