1 Mafumu 21:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita moipitsitsa kutsata mafano, monga mwa zonse amazicita Aamori, amene Yehova adawapitikitsa pamaso pa ana a Israyeli.

1 Mafumu 21

1 Mafumu 21:23-29