1 Mafumu 21:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzalinganiza nyumba yako ndi nyumba ya Yerobiamu mwana wa Nebati, ndi ya Basa mwana wa Ahiya; cifukwa ca kuputa kumene unaputa nako mkwiyo wanga, ndi kucimwitsa Israyeli.

1 Mafumu 21

1 Mafumu 21:12-29