1 Mafumu 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atamva Yezebeli kuti anamponya Naboti miyala nafa, Yezebeli anati kwa Ahabu, Taukani, landirani munda wamphesa wa Naboti Myezreeli uja anakana kukugulitsani ndi ndarama, popeza, Naboti sali ndi moyo, koma wafa.

1 Mafumu 21

1 Mafumu 21:6-21