1 Mafumu 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitatha izi, kunaoneka zotere: Naboti wa ku Yezreeli anali ndi munda wamphesa, unali m'Yezreelimo, m'mbali mwa nyumba ya Ahabu mfumu ya ku Samaria.

1 Mafumu 21

1 Mafumu 21:1-5