1 Mafumu 20:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa mithenga ya Benihadadi, Kauzeni mbuye wanga mfumu, Zonse munayamba kundituma mtumiki wanu kuzifunsa ndidzacita, koma ici sindingacicite. Nicoka mithengayo, nimbwezera mau.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:8-13