1 Mafumu 20:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo otsalawo anathawira ku Afeki kumudzi, ndipo linga linawagwera anthu zikwi makumi awiri mphambu asanu ndi awiri amene adatsalawo. Ndipo Benihadadi anathawa, nalowa m'mudzi, m'cipinda ca m'katimo.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:21-32