1 Mafumu 20:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anawerenga anyamata a akalonga a madera, nawapeza mazana awiri mphambu makumi atatu kudza awiri. Pamenepo anawerenganso anthu onse, ndiwo ana a Israyeli onse zikwi zisanu ndi ziwiri.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:9-18