1 Mafumu 20:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, mneneri anadza kwa Ahabu mfumu ya Israyeli, nati, Atero Yehova, Kodi waona unyinji uwu waukuru wonse? Taonani, ndidzaupereka m'dzanja mwako lero, kuti udziwe kuti ndine Yehova.

1 Mafumu 20

1 Mafumu 20:6-22