1 Mafumu 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ucitire zokoma ana amuna aja a Barizilai wa ku Gileadi, akhale pakati pa akudyera pa gome lako, popeza momwemo amenewo anandiyandikira muja ndinalikuthawa Abisalomu mbale wako.

1 Mafumu 2

1 Mafumu 2:1-9