1 Mafumu 2:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu inalamulira Benaya mwana wa Yehoyada, ndipo iye anaturuka namkwera, namwalira iye. Ndipo ufumu unakhazikika m'dzanja la Solomo.

1 Mafumu 2

1 Mafumu 2:36-46