1 Mafumu 2:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Simeyi ananena ndi mfumu, Mau awa ndi abwino; monga momwe mwanena mbuye wanga mfumu momwemo ndidzacita kapolo wanu. Ndipo Simeyi anakhala m'Yerusalemu masiku ambiri.

1 Mafumu 2

1 Mafumu 2:30-46