1 Mafumu 2:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero mwazi wao udzabweranso pa mutu wace wa Yoabu, ndi pa mutu wa mbumba yace, ku nthawi yamuyaya; koma Davide, ndi mbumba yace, ndi banja lace, ndi mpando wace wacifumu adzakhala ndi mtendere wa Yehova ku nthawi yamuyaya.

1 Mafumu 2

1 Mafumu 2:31-36