1 Mafumu 2:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mbiriyi inamfika Yoabu, pakuti Yoabu anapambukira kwa Adoniya, angakhale sanapambukira kwa Abisalomu. Ndipo Yoabu anathawira ku cihema ca Yehova, nagwira nyanga za guwa la nsembe.

1 Mafumu 2

1 Mafumu 2:26-31