1 Mafumu 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mkaziyo anati, Ndikupemphani kapempho kamodzi, musandikaniza. Ndipo mfumu inati kwa iye, Tapemphani amai wanga, popeza sindikukanizani.

1 Mafumu 2

1 Mafumu 2:17-30