1 Mafumu 19:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atamva Eliya, anapfunda nkhope yace ndi copfunda cace, naturuka, naima pa khomo la phangalo. Ndipo taonani, anamdzera mau akunena naye, Ucitanji kuno, Eliya?

1 Mafumu 19

1 Mafumu 19:8-16