1 Mafumu 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahabu anati kwa Obadiya, Kayendere dziko lonse ku zitsime zonse zamadzi, ndi ku mitsinje yonse, kapena tikapeza msipu ndi kusunga moyo wa akavalo ndi nyuru, zingafe nyama zonse.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:1-11