1 Mafumu 18:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dzanja la Yehova tinakhala pa Eliya; namanga iye za m'cuuno mwace, nathamanga m'tsogolo mwa Ahabu ku cipata ca Yezreeli.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:36-46