1 Mafumu 18:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kacisanu ndi ciwiri anati, Taonani, kwaturuka kunyanja kamtambo konga dzanja la munthu. Nati iye, Kauze Ahabu, kuti, Mangani gareta, tsikani, mvula Ingakutsekerezeni.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:37-46