1 Mafumu 18:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakonza nkhunizo, naduladula ng'ombe, naiika pankhuni. Nati, Dzazani madzi mbiya zinai, muwathire pa nsembe yopsereza ndi pankhuni.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:24-34