1 Mafumu 18:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anatenga ng'ombe ija adawapatsa, naikonza, naitana dzina la Baala, kuyambira m'mawa kufikira pausana, nati, Baala, timvereni ife. Koma panalibe mau kapena wobvomereza. Ndipo anabvinabvina kuguwa adalimanga.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:17-32