1 Mafumu 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya ananena ndi anthuwo, Ine ndatsala ndekha mneneri wa Yehova, koma aneneri a Baala ndiwo anthu mazana anai mphambu makumi asanu.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:15-30