1 Mafumu 18:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono, tumani mundimemezere Aisrayeli onse ku phiri la Karimeli, ndi aneneri a Baala mazana anai mphambu makumi asanu, ndi aneneri a cifanizoco mazana anai, akudya pa gome la Yezebeli.

1 Mafumu 18

1 Mafumu 18:10-27