1 Mafumu 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo makungubwi anamtengera mkate ndi nyama m'mawa, ndi mkate ndi nyama madzulo; namamwa iye mumtsinje.

1 Mafumu 17

1 Mafumu 17:5-10