1 Mafumu 17:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya ananyamula mwanayo, natsika naye ku cipinda cosanja, nalowa naye m'nyumba, nampereka kwa amace; nati Eliya, Taona, mwana wako ali moyo.

1 Mafumu 17

1 Mafumu 17:17-24