1 Mafumu 17:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Ndipo mau a Yehova anadza kwa iye, nati,

3. Coka kuno, nutembenukire kum'mawa, ukabisale kumtsinje Keriti uli ku Yordano.

4. Ndipo kudzakhala kuti uzikamwa mumtsinje, ndipo ndalamulira makungubwi kukudyetsa kumeneko.

1 Mafumu 17