1 Mafumu 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya wa ku Tisibe wokhala ku Gileadi ananena ndi Ahabu, nati, Pali Yehova Mulungu wa Israyeli, amene ndimakhala pamaso pace, ngati adzagwa mame kapena mvula zaka izi, koma ntanena ine ndipo.

1 Mafumu 17

1 Mafumu 17:1-4