1 Mafumu 16:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali monga ngati kunamcepera kuyenda m'macimo a Yerobiamu mwana wa Nebati, iye anakwatira Yezebeli mwana wamkazi wa Etibaala mfumu ya Azidoni, natumikira Baala, namgwadira,

1 Mafumu 16

1 Mafumu 16:26-34