1 Mafumu 16:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nayenda m'njira yonse ya Yerobiamu mwana wa Nebati, ndi chimo lace anacimwitsa nalo Aisrayeli, kuputa mkwiyo wa Yehova Mulungu wa Israyeli ndi zacabe zao.

1 Mafumu 16

1 Mafumu 16:19-27