1 Mafumu 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri ca Asa mfumu ya Yuda, Zimri anali mfumu masiku asanu ndi awiri ku Tiriza. Ndipo anthu analikumangira misasa Gibetoni wa Afilisti.

1 Mafumu 16

1 Mafumu 16:7-21