1 Mafumu 16:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nalowamo Zimri, namkantha, namupha caka ca makomi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri ca Asa mfumu ya Yuda, nalowa ufumu m'malo mwace.

1 Mafumu 16

1 Mafumu 16:3-15