1 Mafumu 15:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo macitidwe ace ena a Abiya, ndi zonse anazicita, kodi sizilembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Yuda? Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobiamu.

1 Mafumu 15

1 Mafumu 15:3-17