1 Mafumu 15:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono Basa mwana wa Ahiya analowa ufumu wa Israyeli caka cacitatu ca Asa mfumu ya Yuda, nakhala mfumu ku Tiriza zaka makomi awiri mphambu zinai.

1 Mafumu 15

1 Mafumu 15:26-34