1 Mafumu 15:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa ca macimo a Yerobiamu, amene adacimwa nao, nacimwitsa nao Aisrayeli, ndi kuutsa kwace kumene anaputa nako mkwiyo wa Yehova Mulungu wa Israyeli.

1 Mafumu 15

1 Mafumu 15:28-34