1 Mafumu 14:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nagona Rehabiamu ndi makolo ace, naikidwa kwa makolo ace m'mudzi wa Davide. Ndipo dzina la amace linali Naama M-amoni, nalowa ufumu m'malo mwace Abiya mwana wace.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:25-31