1 Mafumu 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nacotsa cuma ca m'nyumba ya Yehova, ndi cuma ca m'nyumba ya mfumu; inde anacotsa conseco, nacotsanso zikopa zagolidi zonse adazipanga Solomo.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:17-29