1 Mafumu 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Yehova adzawakantha Aisrayeli monga bango ligwedezeka ndi madzi, nadzazula Aisrayeli m'dziko lino labwino analipatsa makolo ao, nadzawamwazira ku tsidya lija la Firate, popeza iwo anapanga zifanizo zao zokwiyitsa Yehova.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:6-23