1 Mafumu 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aisrayeli onse adzamlira, nadzamuika, popeza iye yekha wa ana a Yerobiamu adzalowa m'manda; pakuti mwa iye mwapezedwa cokoma ca kwa Yehova Mulungu wa Israyeli m'nyumba ya Yerobiamu.

1 Mafumu 14

1 Mafumu 14:5-14