1 Mafumu 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu wa Mulungu ananena ndi mfumu, Mungakhale mundigawira pakati ndi pakati nyumba yanu, sindilowa kwa inu, kapena kudya mkate, kapena kumwa madzi kuno.

1 Mafumu 13

1 Mafumu 13:7-10