1 Mafumu 13:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atacoka iye, mkango unakomana naye panjira, numupha, ndipo mtembo wace unagwera m'njiramo, buru naima pafupi, mkangonso unaima pafupi ndi mtembo.

1 Mafumu 13

1 Mafumu 13:14-29